2 Mafumu 9:36 BL92

36 Nabwerera iwo, namfotokozera. Nati iye, Ndiwo mau a Yehova ananena wo mwa mtumiki wace Eliya wa ku Tisibe, ndi koti, Pa munda wa Yezreeli agaru adzadya mnofu wa Yezebeli;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:36 nkhani