Miyambi 12:10 BL92

10 Wolungama asamalira moyo wa coweta cace;Koma cifundo ca oipa ndi nkhanza.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 12

Onani Miyambi 12:10 nkhani