29 Wosakwiya msanga apambana kumvetsa;Koma wansontho akuza utsiru.
Werengani mutu wathunthu Miyambi 14
Onani Miyambi 14:29 nkhani