8 Nzeru ya wocenjera ndiyo yakuti azindikire njira yace;Koma utsiru wa opusa ndiwo cinyengo.
Werengani mutu wathunthu Miyambi 14
Onani Miyambi 14:8 nkhani