8 Nsembe ya oipa inyansa Yehova;Koma pemphero la oongoka mtima limkondweretsa.
Werengani mutu wathunthu Miyambi 15
Onani Miyambi 15:8 nkhani