Miyambi 22:1 BL92

1 Mbiri yabwino ifunika kopambana cuma cambiri;Kukukomera mtima anzako kuposa siliva ndi golidi.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 22

Onani Miyambi 22:1 nkhani