Miyambi 22:11 BL92

11 Wokonda kuyera mtima,Mfumu idzakhala bwenzi lace cifukwa ca cisomo ca milomo yace.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 22

Onani Miyambi 22:11 nkhani