Miyambi 22:17 BL92

17 Chera makutu ako, numvere mau a anzeru,Nulozetse mtima wako kukadziwa zanga.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 22

Onani Miyambi 22:17 nkhani