Miyambi 24:12 BL92

12 Ukanena, Taonani, sitinadziwa cimeneci;Kodi woyesa mitima sacizindikira ici?Ndi wosunga moyo wako kodi sacidziwa?Ndipo kodi sabwezera munthu yense monga mwa macitidwe ace?

Werengani mutu wathunthu Miyambi 24

Onani Miyambi 24:12 nkhani