11 Ndipo anamuonekera iye mngelo wa Ambuye, naimirira ku dzanja lamanja la guwa la nsembe la zonunkhira.
Werengani mutu wathunthu Luka 1
Onani Luka 1:11 nkhani