Luka 1:15 BL92

15 Pakuti iye adzakhala wamkuru pamaso pa Ambuye, ndipo sadzamwa konse vinyo kapena, kacasu; nadzadzazidwa ndi Mzimu Woyera, kuyambira asanabadwe.

Werengani mutu wathunthu Luka 1

Onani Luka 1:15 nkhani