Luka 1:18 BL92

18 Ndipo Zakariya anati kwa mngelo, Ndidzadziwitsa ici ndi ciani? Pakuti ndine nkhalamba, ndipo zaka zace za mkazi wanga zacuruka.

Werengani mutu wathunthu Luka 1

Onani Luka 1:18 nkhani