Luka 1:27 BL92

27 kwa namwali wopalidwa ubwenzi ndi mwamuna, dzina lace Yosefe, wa pfuko la Davine; ndipo dzina lace la namwaliyo ndilo Mariya.

Werengani mutu wathunthu Luka 1

Onani Luka 1:27 nkhani