Luka 1:34 BL92

34 Koma Mariya anati kwa mngelo, ici cidzacitika bwanji, popeza ine sindidziwa mwamuna?

Werengani mutu wathunthu Luka 1

Onani Luka 1:34 nkhani