Luka 1:38 BL92

38 Ndipo Mariya anati, Onani, mdzakazi wa Ambuye; kukhale kwa ine monga mwa mau anu. Ndipo mngelo anacoka kwa iye.

Werengani mutu wathunthu Luka 1

Onani Luka 1:38 nkhani