Luka 1:66 BL92

66 Ndipo onse amene anazimva anazisunga m'mtima mwao, nanena, Nangamwana uyu adzakhala wotani? Pakuti 13 dzanja la Ambuye linakhala pamodzi ndi iye.

Werengani mutu wathunthu Luka 1

Onani Luka 1:66 nkhani