2 Ndipo ananena kwa iwo, Dzinthu dzicuruka, koma anchito acepa; potero pemphani Mwini dzinthu, kuti akankhe anchito kukututa kwace.
Werengani mutu wathunthu Luka 10
Onani Luka 10:2 nkhani