Luka 10:6 BL92

6 Ndipo mukakhala mwana wa mtendere m'menemo, mtendere wanu udzapumula pa iye; koma ngati mulibe, udzabwerera kwa inu.

Werengani mutu wathunthu Luka 10

Onani Luka 10:6 nkhani