Luka 11:11 BL92

11 Ndipo ndani wa inu ali atate, mwana wace akadzampempha mkate, adzampatsa mwala? kapena nsomba, nadzamninkha njoka m'malo mwa nsomba?

Werengani mutu wathunthu Luka 11

Onani Luka 11:11 nkhani