Luka 11:33 BL92

33 Palibe munthu, atayatsa nyali, aiika m'cipinda capansi, kapena pansi pa muyeso, koma pa coikapo cace, kuti iwo akulowamo aone kuunika.

Werengani mutu wathunthu Luka 11

Onani Luka 11:33 nkhani