39 Koma Ambuye anati kwa iye, Tsopano inu Afarisi muyeretsa kunja kwace kwa cikho ndi mbale, koma m'kati mwanu mudzala zolanda ndi zoipa.
Werengani mutu wathunthu Luka 11
Onani Luka 11:39 nkhani