Luka 11:48 BL92

48 Comweco muli mboni, ndipo mubvomera nchito za makolo anu; cifukwa iwotu anawapha, koma inu muwamangira iwo zapamanda.

Werengani mutu wathunthu Luka 11

Onani Luka 11:48 nkhani