Luka 11:8 BL92

8 Ndinena ndi inu, ngakhale sadzauka ndi kumpatsa, cifukwa ali bwenzi lacevkoma cifukwa ca liuma lace adzauka nadzampatsa iye ziri zonse azisowa.

Werengani mutu wathunthu Luka 11

Onani Luka 11:8 nkhani