Luka 12:15 BL92

15 Ndipo iye anati kwa iwo, Yang'anirani, mudzisungire kupewa msiriro uli wonse; cifukwa moyo wace wa munthu sulingana ndi kucuruka kwa zinthu zace ali nazo.

Werengani mutu wathunthu Luka 12

Onani Luka 12:15 nkhani