Luka 12:20 BL92

20 Koma Mulungu anati kwa iye, Wopusa iwe, usiku womwe uno udzafunidwa moyo wako; ndipo zinthu zimene unazikonza zidzakhala za yani?

Werengani mutu wathunthu Luka 12

Onani Luka 12:20 nkhani