39 Koma zindikirani ici, kuti mwini nyumba akadadziwa nthawi yace yakudza mbala, akadadikira, ndipo sakadalola nyumba yace ibooledwe.
Werengani mutu wathunthu Luka 12
Onani Luka 12:39 nkhani