Luka 13:2 BL92

2 Ndipo iye anayankha nati kwa iwo, Kodi muyesa kuti Agalileya aja anali anthu akucimwa koposa Agalileya onse, cifukwa anamva zowawa izi?

Werengani mutu wathunthu Luka 13

Onani Luka 13:2 nkhani