Luka 13:21 BL92

21 Ufanana ndi cotupitsa mikate, cimene mkazianatenga, nacibisa mu miyeso itatu ya ufa, kufikira unatupa wonsewo,

Werengani mutu wathunthu Luka 13

Onani Luka 13:21 nkhani