Luka 14:17 BL92

17 ndipo anatumiza kapolo wace pa nthawi ya phwando kukanena kwa oitanidwawo, idzani, cifukwa zonse zakonzeka tsopano.

Werengani mutu wathunthu Luka 14

Onani Luka 14:17 nkhani