Luka 14:20 BL92

20 Ndipo anati wina, Ine ndakwatira mkazi, ndipo cifukwa cace sindingathe kudza.

Werengani mutu wathunthu Luka 14

Onani Luka 14:20 nkhani