23 Ndipo mbuye ananena kwa kapoloyo, Turuka, nupite kumiseu ndi njira za kuminda, nuwaumirize anthu alowe, kuti nyumba yanga idzale.
Werengani mutu wathunthu Luka 14
Onani Luka 14:23 nkhani