Luka 14:5 BL92

5 Ndipo anati kwa iwo, Ndani wa inu buru wace kapena ng'ombe yace itagwa m'citsime, ndipo sadzaiturutsa pomwepo tsiku la Sabata kodi?

Werengani mutu wathunthu Luka 14

Onani Luka 14:5 nkhani