12 ndipo wamng'onoyo anati kwa atate wace, Atate, ndigawirenitu zanga za pa cuma canu. Ndipo iye anawagawira za moyo wace.
Werengani mutu wathunthu Luka 15
Onani Luka 15:12 nkhani