Luka 15:27 BL92

27 Ndipo uyu anati kwa iye, Mng'ono wako wafika; ndipo atate wako anapha mwana wa ng'ombe wonenepa, cifukwa anamlandira iye wamoyo.

Werengani mutu wathunthu Luka 15

Onani Luka 15:27 nkhani