Luka 15:6 BL92

6 Ndipo pakufika kunyumba kwace amema abwenzi ace ndi anansi ace, nanena nao, Kondwerani ndi ine, cifukwa ndinapeza nkhosa yanga yotayikayo.

Werengani mutu wathunthu Luka 15

Onani Luka 15:6 nkhani