9 Ndipo m'mene aipeza amema abwenzi ace ndi anansi ace, nanena; Kondwerani ndi ine, cifukwa ndinapeza ndalama ndidatayayo.
Werengani mutu wathunthu Luka 15
Onani Luka 15:9 nkhani