10 Cotero Inunso m'mene mutacita zonse anakulamulirani, Denani, Ife ndife akapolo opanda pace, tangocita zimene tayenera kuzicita.
Werengani mutu wathunthu Luka 17
Onani Luka 17:10 nkhani