27 Anadya, anamwa, anakwatira, anakwatiwa, kufikira tsiku lija Nowa analowa m'cingalawa, ndipo cinadza cigumula, niciwaononga onsewo.
Werengani mutu wathunthu Luka 17
Onani Luka 17:27 nkhani