3 Kadzicenjerani nokha; akacimwa mbale wako umdzudzule; akalapa, umkhululukire.
Werengani mutu wathunthu Luka 17
Onani Luka 17:3 nkhani