Luka 18:24 BL92

24 Ndipo Yesu pomuona iye anati, Ha! nkubvutika nanga kwa anthu eni cuma kulowa Ufumu wa Mulungu!

Werengani mutu wathunthu Luka 18

Onani Luka 18:24 nkhani