Luka 18:9 BL92

9 Ndipo anatinso kwa ena amene anadzikhulupirira mwa iwo okha kuti ali olungama, napeputsa onse ena, fanizo ili,

Werengani mutu wathunthu Luka 18

Onani Luka 18:9 nkhani