Luka 19:17 BL92

17 Ndipo anati kwa iye, Cabwino, kapolo wabwino iwe; popeza unakhala wokhulupirika m'cacing'onong'ono, khala nao ulamuliro pa midzi khumi.

Werengani mutu wathunthu Luka 19

Onani Luka 19:17 nkhani