Luka 19:26 BL92

26 Ndinena ndi inu, kuti kwa yense wakukhala naco kudzapatsidwa; koma kwa iye amene alibe kanthu, cingakhale cimene ali naco cidzacotsedwa.

Werengani mutu wathunthu Luka 19

Onani Luka 19:26 nkhani