38 nanena, Wolemekezeka Mfumuyo ikudza m'dzina la Ambuye; mtendere m'Mwamba, ndi ulemerero m'Mwambamwamba.
Werengani mutu wathunthu Luka 19
Onani Luka 19:38 nkhani