21 Ndipo pamene panakwanira masiku asanu ndi atatu akumdula iye, anamucha dzina lace Yesu, limene anachula mngeloyo asanalandiridwe iye m'mimba.
Werengani mutu wathunthu Luka 2
Onani Luka 2:21 nkhani