27 Ndipo iye analowa kuKacisi ndi Mzimu: ndipo pamene atate ndi amace analowa ndi kamwanako Yesu, kudzamcitira iye mwambo wa cilamulo,
Werengani mutu wathunthu Luka 2
Onani Luka 2:27 nkhani