Luka 2:44 BL92

44 koma iwo anayesa kuti iye ali m'cipiringu ca ulendo, nayenda ulendo wa tsiku limodzi; ndipo anayamba kumfunafuna iye mwa abale ao ndi mwa anansi ao;

Werengani mutu wathunthu Luka 2

Onani Luka 2:44 nkhani