Luka 2:49 BL92

49 Ndipo iye anati kwa iwo, Kuli bwanji kuti munalikundifunafuna Ine? Simunadziwa kodi kuti kundiyenera Ine 5 ndikhale m'zace za Atate wanga?

Werengani mutu wathunthu Luka 2

Onani Luka 2:49 nkhani