Luka 20:13 BL92

13 Ndipo mwini mundawo anati, Ndidzacita ciani? Ndidzatuma mwana wanga amene ndikondana naye; kapena akamcitira iye ulemu.

Werengani mutu wathunthu Luka 20

Onani Luka 20:13 nkhani