Luka 20:17 BL92

17 Koma iye anawapenyetsa iwo, nati, Nciani ici cinalembedwa,Mwala umene anaukana omanga nyumba,Womwewu unakhala mutu wa pangondya.

Werengani mutu wathunthu Luka 20

Onani Luka 20:17 nkhani